Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yoswa 10:30 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ndipo Yehova anapereka uwunso, ndi mfumu yace m'dzanja la Israyeli; ndipo anaukantha ndi lupanga lakuthwa, ndi amoyo onse anali m'mwemo, osasiyamo ndi mmodzi yense; namcitira mfumu yace monga anacitira mfumu ya ku Yeriko.

Werengani mutu wathunthu Yoswa 10

Onani Yoswa 10:30 nkhani