Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yoswa 10:28 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Yoswa anagwira Makeda tsiku lomwe lija ndi kuukantha ndi lupanga lakuthwa, ndi mfumu yace yom we; anawaononga konse, ndi amoyo onse anali m'mwemo, osasiyapo ndi mmodzi yense, nacitira mfumu ya ku Makeda monga anacitira mfumu ya ku Yeriko.

Werengani mutu wathunthu Yoswa 10

Onani Yoswa 10:28 nkhani