Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yoswa 10:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo kunali, pamene Adoni-Zedeki mfumu ya Yerusalemu anamva kuti Yoswa adalanda Ai, ndi kumuononga konse; nacitira Ai ndi mfumu yace monga adacitira Yeriko ndi mfumu yace; ndi kuti nzika za Gibeoni zinacitirana mtendere ndi Israyeli, nizikhala pakati pao;

Werengani mutu wathunthu Yoswa 10

Onani Yoswa 10:1 nkhani