Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yoswa 1:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Kodi sindinakulamulira iwe? Khala wamphamvu, nulimbike mtima, usaope, kapena kutenga nkhawa, pakuti Yehova Mulungu wako ali ndi iwe kuli konse umukako.

Werengani mutu wathunthu Yoswa 1

Onani Yoswa 1:9 nkhani