Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yona 4:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo kunali, poturuka dzuwa Mulungu anaika mphepo ya kum'mawa yotentha, ndipo dzuwa linatentha mutu wace wa Yona, nalefuka iye, nadzipempherera kuti afe; nati, Kundikomera ine kufa, kukhala ndi moyo ai.

Werengani mutu wathunthu Yona 4

Onani Yona 4:8 nkhani