Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yona 4:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anapemphera kwa Yehova, nati, Ha, Yehova! si ndiwo mau anga ndikali m'dziko langa? cifukwa cace ndinafulumira kuthawira ku Tarisi, pakuti ndinadziwa kuti Inu ndinu Mulungu wacisomo ndi wodzala cifundo, wolekerera ndi wokoma mtima mocuruka, ndi woleka coipaco.

Werengani mutu wathunthu Yona 4

Onani Yona 4:2 nkhani