Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yona 1:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma Yona ananyamuka kuti athawire ku Tarisi, kuzemba Yehova; ndipo anatsikira ku Yopa, napezako combo comuka ku Tarisi, napereka ndalama zace, natsikira m'menemo, kuti apite nao ku Tarisi kuzemba Yehova.

Werengani mutu wathunthu Yona 1

Onani Yona 1:3 nkhani