Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yobu 9:1-3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Pamenepo Yobu anayankha, nati,

2. Zoona, ndidziwa kuti ciri cotero.Koma munthu adzakhala walungama bwanji kwa Mulungu?

3. Akafuna Iye kutsutsana naye,Sadzambwezera Iye mau amodzi onse mwa cikwi.

Werengani mutu wathunthu Yobu 9