Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yobu 7:1-3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Kodi munthu alibe nkhondo kunja kuno?Kodi masiku ace sakunga masiku a wolembedwa nchito?

2. Monga kapolo woliralira mthunzi,Monga wolembedwa nchito ayembekezera mphotho yace,

3. Momwemo anandilowetsa miyezi yopanda pace.Nandiikiratu zowawa usiku ndi usiku.

Werengani mutu wathunthu Yobu 7