Ndani uyu abisa uphungu wosadziwa kanthu?Cifukwa cace ndinafotokozera zimene sindinazizindikira,Zondidabwiza, zosazidziwa ine,