Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yobu 42:15-17 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

15. Ndipo m'dziko monse simunapezeka akazi okongola ngati ana akazi a Yobu, nawapatsa colowa atate wao pamodzi ndi alongo ao.

16. Ndipo zitatha izi, Yobu anakhala ndi moyo zaka zana limodzi mphambu makumi anai, naona ana ace ndi zidzukulu zace mibadwo inai.

17. Namwalira Yobu, wokalamba ndi wa masiku ocuruka.

Werengani mutu wathunthu Yobu 42