Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yobu 41:5-7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

5. Kodi udzasewera nayo ngati mbalame?Kapena udzaimangira anamwali ako kuti aiwete?

6. Kodi opangana malonda adzaitsatsa?Adzaigawana eni malonda?

7. Kodi udzadzaza khungu lace ndi nchetho,Kapena mutu wace ndi miomba?

Werengani mutu wathunthu Yobu 41