Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yobu 41:31-33 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

31. Icititsa nthubwinthubwi pozama ngati nkhali,Isanduliza nyanja ikunge mafuta.

32. Icititsa mifunde yonyezimira pambuyo pace;Munthu akadati pozama pali ndi imvi.

33. Pa dziko lapansi palibe cina colingana nayo,Colengedwa copanda mantha.

Werengani mutu wathunthu Yobu 41