Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yobu 41:20-23 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

20. M'mphuno mwace muturuka utsi,Ngati nkhali yobwadamuka ndi moto wa zinyatsi.

21. Mpweya wace uyatsa makara,Ndi m'kamwa mwace muturuka lawi la moto.

22. Kukhosi kwace kukhala mphamvu,Ndi mantha abvumbuluka patsogolo pace,

23. Nyama yace yopsapsala igwiranaIkwima pathupi pace yosagwedezeka.

Werengani mutu wathunthu Yobu 41