Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yobu 40:21-23 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

21. Igona pansi patsinde pa mitengo yamthunzi,Pobisala pabango ndi pathawale.

22. Mitengo yamthunzi iiphimba ndi mthunzi wao,Misondodzi ya kumtsinje iizinga.

23. Taona madzi a mumtsinje akakula, siinjenjemera;Ilimbika mtima, ngakhale Yordano atupa mpaka pakamwa pace,

Werengani mutu wathunthu Yobu 40