Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yobu 4:14-16 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

14. Anandidzera mantha ndi kunjenjemera,Nanthunthumira nako mafupa anga onse.

15. Pamenepo panapita mzimu pamaso panga;Tsitsi la thupi langa lidati nyau nyau.

16. Unaima ciriri, koma sindinatha kuzindikira maonekedwe ace;Panali mzukwa pamaso panga;Kunali cete, ndipo ndidamva mau akuti,

Werengani mutu wathunthu Yobu 4