Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yobu 39:19-22 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

19. Wampatsa kavalo mphamvu yace kodi?Wambveka pakhosi pace cenjerere cogwedezeka?

20. Wamlumphitsa kodi ngati dzombe?Ulemerero wa kumina kwace ngwoopsa.

21. Apalasa kucigwa, nakondwera nayo mphamvu yace;Aturuka kukomana nao eni zida.

22. Aseka mantha osaopsedwa,Osabwerera kuthawa lupanga.

Werengani mutu wathunthu Yobu 39