Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yobu 38:38-40 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

38. Pokandika pfumbi,Ndi kuundana zibuma pamodzi?

39. Kodi ukhoza kusakira mkango waukazi nyama?Ndi kukwaniritsa cakudya ca misona,

40. Pamene ibwathama m'ngaka mwao,Nikhala mobisala kulaliramo?

Werengani mutu wathunthu Yobu 38