Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yobu 37:8-11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

8. Pamenepo zirombo zilowa mobisalamo,Nizikhala m'ngaka mwao.

9. M'cipinda mwace muturuka kabvumvulu,Ndi cisanu cifuma kumpoto.

10. Mwa kupuma kwace apereka cipale,Ndi madzi acitando aundana.

11. Asenzetsanso mtambo wakuda bii madzi,Afunyulula mtambo wokhalamo mphezi yace;

Werengani mutu wathunthu Yobu 37