Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yobu 37:7-10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

7. Atsekereza mokhomera cizindikilo dzanja la munthu ali yense,Kuti anthu onse anawalenga adziwe.

8. Pamenepo zirombo zilowa mobisalamo,Nizikhala m'ngaka mwao.

9. M'cipinda mwace muturuka kabvumvulu,Ndi cisanu cifuma kumpoto.

10. Mwa kupuma kwace apereka cipale,Ndi madzi acitando aundana.

Werengani mutu wathunthu Yobu 37