Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yobu 37:22-24 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

22. Kucokera kumpoto kudzera kuwala konyezimira,Mulungu ali nao ukulu woopsa.

23. Kunena za Wamphamvuyonse, sitingamsanthule; ndiye wa mphamvu yoposa;Koma mwa ciweruzo ndi cilungamo cocuruka samasautsa.

24. M'mwemo anthu amuopa,Iye sasamalira ali yense wanzeru mumtima.

Werengani mutu wathunthu Yobu 37