Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yobu 36:30-32 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

30. Taonani, Iye ayala kuunika kwace pamenepo.Nabvundikira kunsi kwace kwa nyanja.

31. Pakuti aweruza nazo mitundu ya anthu.Apatsa cakudya cocuruka.

32. Akutidwa manja ace ndi mphezi,Nailamulira igwere pofunapo Iye.

Werengani mutu wathunthu Yobu 36