Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yobu 36:1-4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Elihu nabwereza, nati,

2. Mundilole pang'ono, ndidzakuuzani,Pakuti ndiri naonso mau akunenera Mulungu.

3. Ndidzatenga nzeru zanga kutali,Ndidzabvomereza kuti Mlengi wanga ndi wolungama.

4. Pakuti zoonadi, mau anga sali abodza,Wakudziwitsa mwangwiro ali nanu.

Werengani mutu wathunthu Yobu 36