Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yobu 34:25-28 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

25. Pakuti asamalira nchito zao,Nawagubuduza usiku kuti aphwanyike.

26. Awakantha ngati oipa,Poyera pamaso pa anthu.

27. Popeza anapambuka, naleka kumtsata,Osasamalira njira zace ziri zonse.

28. M'mwemo anafikitsa kwa Iye kupfuula kwa osauka;Ndipo anamva Iye kupfuula kwa ozunzika.

Werengani mutu wathunthu Yobu 34