Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yobu 33:30-33 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

30. Kumbweza angalowe kumanda,Kuti kuunika kwa moyo kumuwalire.

31. Cherani khutu, Yobu, mundimvere ine;Mukhale cete, ndipo ndidzanena ine.

32. Ngati muli nao mau mundiyankhe.Nenani, pakuti ndifuna kukulungamitsani.

33. Ngati mulibe mau, tamverani Ine;Mukhale cete, ndipo ndizakuphunzitsani nzeru.

Werengani mutu wathunthu Yobu 33