Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yobu 33:16-18 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

16. Pamenepo atsegula makutu a anthu,Nakomera cizindikilo cilangizo cao;

17. Kuti acotse munthu ku cimene akadacita,Ndi kubisira munthu kudzikuza kwace;

18. Kuti amletse angaonongeke,Ndi moyo wace ungatayike ndi lupanga.

Werengani mutu wathunthu Yobu 33