Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yobu 31:38-40 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

38. Ngati minda yanga ipfuula monditsutsa,Ndi nthumbira zace zilira pamodzi;

39. Ngati ndadya zipatso zace wopanda ndarama,Kapena kutayitsa eni ace moyo wao;

40. Imere minga m'malo mwa tirigu,Ndi dawi m'malo mwa barele.Mau a Yobu atha.

Werengani mutu wathunthu Yobu 31