Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yobu 28:1-2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Koma kuli mtapo wa siliva, Ndi malo a golidi amene amuyenga.

2. Citsulo acitenga m'nthaka,Ndi mkuwa ausungunula kumwala.

Werengani mutu wathunthu Yobu 28