Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yobu 25:4-6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

4. Potero munthu akhala bwanji wolungama kwa Mulungu?Kapena wobadwa ndi mkazi akhala woyera bwanji?

5. Taonani, ngakhale mwezi ulibe kuwala;Ndi nyenyezi siziyera pamaso pace;

6. Kopambana kotani nanga munthu, ndiye mphutsi!Ndi wobadwa ndi munthu, ndiyo nyongolotsi!

Werengani mutu wathunthu Yobu 25