Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yobu 25:3-5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

3. Ngati awerengedwa makamu ace?Ndipo ndaniyo, kuunika kwace sikumturukira?

4. Potero munthu akhala bwanji wolungama kwa Mulungu?Kapena wobadwa ndi mkazi akhala woyera bwanji?

5. Taonani, ngakhale mwezi ulibe kuwala;Ndi nyenyezi siziyera pamaso pace;

Werengani mutu wathunthu Yobu 25