Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yobu 25:1-3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Pamenepo Bilidadi wa ku Suki anayankha, nati,

2. Kulamulira ndi kuopsa kuti ndi Iye;Acita mtendere pa zam'mwamba zace.

3. Ngati awerengedwa makamu ace?Ndipo ndaniyo, kuunika kwace sikumturukira?

Werengani mutu wathunthu Yobu 25