Yobu 21:1-4 Buku Lopatulika 1992 (BL92) Pamenepo Yobu anayankha, nati, Kodi ine, kudandaula kwanga, ndidandaulira munthu?Ndipo ndilekerenji kupsa mtima?