Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yobu 20:27-29 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

27. M'mwamba mudzabvumbulutsa mphulupulu yace,Ndi dziko lapansi lidzamuukira.

28. Phindu la m'nyumba mwace lidzacoka,Akatundu ace adzamthawa tsiku la mkwiyo wace.

29. Ili ndi gawo la munthu woipa, locokera kwa Mulungu,Ndi colowa amuikiratu Mulungu.

Werengani mutu wathunthu Yobu 20