Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yobu 20:1-6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Pamenepo anayankha Zofari Mnaama, nati,

2. M'mwemo zolingirira zanga zindiyankha,Cifukwa cace ndifulumidwa m'kati mwanga.

3. Ndamva kudzudzula kwakundicititsa manyazi,Ndi mzimu wa nzeru yanga undiyankha.

4. Kodi sucidziwa ici ciyambire kale lomwe,Kuyambira anaika munthu pa dziko lapansi,

5. Kuti kupfuula kokondwera kwa woipa sikukhalira kutha,Ndi cimwemwe ca wonyoza Mulungu cikhala kamphindi?

6. Cinkana ukulu wace ukwera kumka kuthambo,Nugunda pamitambo mutu wace;

Werengani mutu wathunthu Yobu 20