Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yobu 20:1-3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Pamenepo anayankha Zofari Mnaama, nati,

2. M'mwemo zolingirira zanga zindiyankha,Cifukwa cace ndifulumidwa m'kati mwanga.

3. Ndamva kudzudzula kwakundicititsa manyazi,Ndi mzimu wa nzeru yanga undiyankha.

Werengani mutu wathunthu Yobu 20