Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yobu 18:12-14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

12. Njala idzatha mphamvu yace,Ndi tsoka lidzamkonzekeratu pambali pace.

13. Zidzatha ziwalo za thupi lace,Mwana woyamba wa imfa adzatha ziwalo zace.

14. Adzazulidwa kuhema kwace kumene anakhulupirira;Nadzatengedwa kumka naye kwa mfumu ya zoopsa.

Werengani mutu wathunthu Yobu 18