Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yobu 16:20-22 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

20. Mabwenzi anga andinyoza; Koma diso langa lilirira misozi kwa Mulungu;

21. Ha! munthu akadapembedzera mnzace kwa Mulungu,Monga munthu apembedzera mnansi wace!

22. Pakuti zitafika zaka zowerengeka,Ndidzamuka ku njira imene sindibwererako.

Werengani mutu wathunthu Yobu 16