Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yobu 11:18-20 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

18. Ndipo udzalimbika mtima popeza pali ciyembekezo;Nudzafunafuna, ndi kugona mosatekeseka,

19. Inde udzagona pansi, wopanda wina wakukunjenjemeretsa,Ndipo ambiri adzakupembedza,

20. Koma maso a oipa adzagoma, Ndi pothawirapo padzawasowa,Ndipo ciyembekezo cao ndico kupereka mzimu wao.

Werengani mutu wathunthu Yobu 11