Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yobu 1:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo kunatero, atatha masiku a madyererowa Yobu anatumiza mau, nawapatula, nauka mamawa, nafukiza nsembe zopsereza, monga mwa kuwerenga kwa iwo onse; pakuti Yobu anati, Kapena anacimwa ana anga, nacitira Mulungu mwano m'mtima mwao. Anatero Yobu masiku onse.

Werengani mutu wathunthu Yobu 1

Onani Yobu 1:5 nkhani