Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yobu 1:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Zoweta zacenso zinali nkhosa zikwi zisanu ndi ziwiri, ndi ngamila zikwi zitatu, ndi ng'ombe zamagoli mazana asanu, ndi aburu akazi mazana asanu, anchito ace omwe ndi ambiri; cotero munthuyu anaposa anthu onse'a kum'mawa.

Werengani mutu wathunthu Yobu 1

Onani Yobu 1:3 nkhani