Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 9:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti kwa ife mwana wakhanda wabadwa, kwa ife mwana wamwamuna wapatsidwa; ndipo ulamuliro udzakhala pa phewa lace, ndipo adzamucha dzina lace Wodabwitsa, Wauphungu, Mulungu wamphamvu, Atate Wosatha, Kalonga wa mtendere.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 9

Onani Yesaya 9:6 nkhani