Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 9:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma kumene kunali nsautso sikudzakhala kuziya. Poyamba paja Mulungu ananyozetsa dziko la Zebuloni, ndi dziko la Naftali, koma potsiriza pace Iye analicitira ulemu, pa khwalala la kunyanja, patsidya pa Yordano, Galileya wa amitundu.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 9

Onani Yesaya 9:1 nkhani