Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 7:25 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo zitunda zonse zinalimidwa ndi khasu, iwe sudzafikako cifukwa ca kuopa lunguzi ndi minga, koma pomwepo padzakhala potumizira ng'ombe ndi popondaponda nkhosa.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 7

Onani Yesaya 7:25 nkhani