Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 66:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo mudzaciona, ndipo mtima wanu udzasangalala, ndipo mafupa anu adzakula ngati msipu; ndipo dzanja la Yehova lidzadziwika ndi atumiki ace, ndipo adzakwiyira adani ace.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 66

Onani Yesaya 66:14 nkhani