Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 65:25 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Mmbulu ndi mwana wa nkhosa zidzadyera pamodzi; ndi mkango udzadya udzu ngati ng'ombe; ndi pfumbi lidzakhala cakudya ca njoka; sizidzapwetekana, kapena kusakazana m'phiri langa lonse lopatulika, ati Yehova.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 65

Onani Yesaya 65:25 nkhani