Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 65:16 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

comweco iye amene adzidalitsa yekha m'dziko lapansi, adzadzidalitsa yekha mwa Mulungu woona; ndipo iye amene alumbira m'dziko lapansi adzalumbira pa Mulungu woona; popeza zobvuta zoyamba zaiwalika, ndi popeza zabisalika kumaso kwanga.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 65

Onani Yesaya 65:16 nkhani