Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 63:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndaponda ndekha mopondera mphesa, ndipo panalibe nane mmodzi wa mitundu ya anthu; inde ndinawaponda m'kukwiya kwanga, ndi kuwapondereza mu ukali wanga: ndi mwazi wa moyo wao unawazidwa pa zobvala zanga; ndipo ndadetsa copfunda canga conse.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 63

Onani Yesaya 63:3 nkhani