Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 63:18-19 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

18. Anthu anu opatulika anakhala naco kanthawi kokha; adani athu apondereza kacisi wanu wopatulika.

19. Ife takhala ngati iwo amene simunawalamulira konse, ngati iwo amene sanachedwa dzina lanu.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 63