Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 63:16 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti Inu ndinu Atate wathu, ngakhale Abrahamu satidziwa ife, ndi Israyeli satizindikira ife. Inu Yehova ndinu Atate wathu, Mombolo wathu wacikhalire ndi dzina lanu.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 63

Onani Yesaya 63:16 nkhani