Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 63:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo iwo anakumbukira masiku akale, Mose ndi anthu ace, nati, Ali kuti Iye amene anawaturutsa m'nyanja pamodzi ndi abusa a gulu lace? Ali kuti Iye amene anaika mzimu wace woyera pakati pao,

Werengani mutu wathunthu Yesaya 63

Onani Yesaya 63:11 nkhani